Police houses, Mangochi
Tawonani kukongola kwa nyumba zanyuwani za apolisi uko ku Malemia Camp ku Malindi, boma la Mangochi. Ndithutu apolisi athu nawo adzikhala munyumba zolemekezeka, zokongola komanso za zipangizo zamakono mkati.Kwantere ndithu Dr. Lazarus Chakwera akuwonetsetsa kuti miyoyo ya apolisi, asilikali ndi onse ogwira ntchito zachitetezo mudziko lino isinthe. Pa ground pakuwala!